|
|
|
|
Cholinga cha kampani ya NAVEX ndi kuonetsetsa kuti inu mutha kuyankhulana nkhani ndi nkhawa zokhudza mchitidwe osayenera kapena osaloledwa pakati pa akuluakulu oyendetsa ntchito za bungwe kapena komiti yaikulu yoyang'anira ntchito za bungwe, ndi kuti mukutha kuyankhula zimenezi motetezeka komanso mwachilungamo popanda inu kudziwika kuti ndinu mwapanga zimenezi. |
|